Yohane 11:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Inde, ndikudziwa kuti mumandimva nthawi zonse, koma ndikunena izi chifukwa cha khamu la anthu+ aimirira panowa, kuti akhulupirire kuti inu munandituma ine.”+
42 Inde, ndikudziwa kuti mumandimva nthawi zonse, koma ndikunena izi chifukwa cha khamu la anthu+ aimirira panowa, kuti akhulupirire kuti inu munandituma ine.”+