Luka 12:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Komanso ndikukuuzani ndithu, mabwenzi anga,+ Musamaope amene amapha thupi lokha, amene sangathe kuchita zoposa pamenepa.+
4 Komanso ndikukuuzani ndithu, mabwenzi anga,+ Musamaope amene amapha thupi lokha, amene sangathe kuchita zoposa pamenepa.+