Salimo 93:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Zikumbutso zanu ndi zodalirika zedi.+Chiyero ndi choyenera nyumba yanu+ mpaka muyaya, inu Yehova.+ Luka 2:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Koma iye anawayankha kuti: “Mumandifunafuna chifukwa chiyani? Kodi simunadziwe kuti ndiyenera kupezeka m’nyumba ya Atate wanga?”+
49 Koma iye anawayankha kuti: “Mumandifunafuna chifukwa chiyani? Kodi simunadziwe kuti ndiyenera kupezeka m’nyumba ya Atate wanga?”+