Salimo 26:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova, ine ndimakonda nyumba imene inu mumakhala+Ndi malo amene kumakhala ulemerero wanu.+ Salimo 27:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chinthu chimodzi chimene ndapempha kwa Yehova,+Chimenecho ndi chimene ndimachikhumba,+N’chakuti, ndikhale m’nyumba ya Yehova masiku onse a moyo wanga,+Kuti ndione ubwino wa Yehova,+Komanso kuti ndiyang’ane kachisi wake moyamikira.+ Miyambo 20:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ngakhale mnyamata amadziwika ndi ntchito zake, ngati zochita zake zili zoyera ndiponso zowongoka.+ Yohane 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Tsopano anauza ogulitsa nkhundawo kuti: “Chotsani izi muno! Mulekeretu kusandutsa nyumba+ ya Atate wanga kukhala nyumba ya malonda!”+
4 Chinthu chimodzi chimene ndapempha kwa Yehova,+Chimenecho ndi chimene ndimachikhumba,+N’chakuti, ndikhale m’nyumba ya Yehova masiku onse a moyo wanga,+Kuti ndione ubwino wa Yehova,+Komanso kuti ndiyang’ane kachisi wake moyamikira.+
11 Ngakhale mnyamata amadziwika ndi ntchito zake, ngati zochita zake zili zoyera ndiponso zowongoka.+
16 Tsopano anauza ogulitsa nkhundawo kuti: “Chotsani izi muno! Mulekeretu kusandutsa nyumba+ ya Atate wanga kukhala nyumba ya malonda!”+