Salimo 58:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Oipa akhala opotoka maganizo kuyambira ali m’mimba.+Iwo asochera kuyambira ali m’mimba,Ndipo amalankhula zabodza.+ Miyambo 22:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Uchitsiru umakhazikika mumtima mwa mwana.+ Koma ndodo yomulangira* ndi imene imauthamangitsira kutali ndi iye.+ Mateyu 7:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Momwemonso mtengo uliwonse wabwino umabala zipatso zabwino, koma mtengo uliwonse wovunda umabala zipatso zopanda pake.+ Luka 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 chifukwa adzakhala wamkulu pamaso pa Yehova.+ Koma asadzamwe vinyo ngakhale pang’ono+ kapena chakumwa chaukali chilichonse. Ndipo adzadzazidwa ndi mzimu woyera kuyambira ali m’mimba mwa mayi ake.+
3 Oipa akhala opotoka maganizo kuyambira ali m’mimba.+Iwo asochera kuyambira ali m’mimba,Ndipo amalankhula zabodza.+
15 Uchitsiru umakhazikika mumtima mwa mwana.+ Koma ndodo yomulangira* ndi imene imauthamangitsira kutali ndi iye.+
17 Momwemonso mtengo uliwonse wabwino umabala zipatso zabwino, koma mtengo uliwonse wovunda umabala zipatso zopanda pake.+
15 chifukwa adzakhala wamkulu pamaso pa Yehova.+ Koma asadzamwe vinyo ngakhale pang’ono+ kapena chakumwa chaukali chilichonse. Ndipo adzadzazidwa ndi mzimu woyera kuyambira ali m’mimba mwa mayi ake.+