Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 3:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Nyale ya Mulungu inali isanazimitsidwe, ndipo Samueli anali atagona m’kachisi+ wa Yehova, mmene munali likasa la Mulungu.

  • 1 Mbiri 16:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Motero analowetsa+ likasa la Mulungu woona muhema limene Davide anamanga, n’kuika likasalo pamalo ake muhemalo.+ Kenako iwo anapereka nsembe zopsereza ndi nsembe zachiyanjano kwa Mulungu woona.+

  • Salimo 27:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Chinthu chimodzi chimene ndapempha kwa Yehova,+

      Chimenecho ndi chimene ndimachikhumba,+

      N’chakuti, ndikhale m’nyumba ya Yehova masiku onse a moyo wanga,+

      Kuti ndione ubwino wa Yehova,+

      Komanso kuti ndiyang’ane kachisi wake moyamikira.+

  • Salimo 84:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pakuti kukhala tsiku limodzi m’mabwalo anu n’kwabwino kuposa kukhala masiku 1,000 kwina.+

      Ndasankha kuima pakhomo la nyumba ya Mulungu wanga+

      Kuposa kukhala m’mahema a anthu oipa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena