1 Yohane 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Taganizirani za chikondi chachikulu+ chimene Atate watisonyeza. Watitchula kuti ndife ana a Mulungu,+ ndipo ndifedi ana ake. N’chifukwa chake dziko+ silitidziwa, pakuti silimudziwa iyeyo.+
3 Taganizirani za chikondi chachikulu+ chimene Atate watisonyeza. Watitchula kuti ndife ana a Mulungu,+ ndipo ndifedi ana ake. N’chifukwa chake dziko+ silitidziwa, pakuti silimudziwa iyeyo.+