Mateyu 12:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Komanso, ngati ine ndimatulutsa ziwanda ndi mphamvu ya Belezebule,+ nanga otsatira anu amazitulutsa ndi mphamvu ya ndani? Pa chifukwa ichi, iwo adzakuweruzani.
27 Komanso, ngati ine ndimatulutsa ziwanda ndi mphamvu ya Belezebule,+ nanga otsatira anu amazitulutsa ndi mphamvu ya ndani? Pa chifukwa ichi, iwo adzakuweruzani.