Machitidwe 16:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mtsikana ameneyu anali kumangotsatira Paulo ndi ife n’kumafuula kuti:+ “Anthu awa ndi akapolo a Mulungu Wam’mwambamwamba, ndipo akulengeza njira ya chipulumutso kwa inu.”
17 Mtsikana ameneyu anali kumangotsatira Paulo ndi ife n’kumafuula kuti:+ “Anthu awa ndi akapolo a Mulungu Wam’mwambamwamba, ndipo akulengeza njira ya chipulumutso kwa inu.”