Chivumbulutso 18:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Amalonda oyendayenda+ a zinthu zimenezi, amene analemerera pa iye, adzaima patali chifukwa cha mantha poona kuzunzika kwake. Iwo adzamulira maliro ndi kumva chisoni+
15 “Amalonda oyendayenda+ a zinthu zimenezi, amene analemerera pa iye, adzaima patali chifukwa cha mantha poona kuzunzika kwake. Iwo adzamulira maliro ndi kumva chisoni+