Miyambo 15:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Munthu wopsa mtima amayambitsa mkangano,+ koma munthu wosakwiya msanga amaziziritsa mkangano.+