Machitidwe 21:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Choncho titatsiriza masikuwo, tinanyamuka kuti tipitirize ulendo wathu. Ndipo abale onse, pamodzi ndi amayi ndi ana, anatiperekeza mpaka kunja kwa mzindawo. Kumeneko tinagwada+ pagombe ndi kupemphera
5 Choncho titatsiriza masikuwo, tinanyamuka kuti tipitirize ulendo wathu. Ndipo abale onse, pamodzi ndi amayi ndi ana, anatiperekeza mpaka kunja kwa mzindawo. Kumeneko tinagwada+ pagombe ndi kupemphera