Machitidwe 5:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Koma mwamuna wina anaimirira pa Khoti Lalikulu la Ayuda. Iyeyu anali Mfarisi wotchedwa Gamaliyeli,+ mphunzitsi wa Chilamulo wolemekezedwa ndi anthu onse. Ndiyeno analamula kuti anthuwo awatulutse kwa kanthawi.+
34 Koma mwamuna wina anaimirira pa Khoti Lalikulu la Ayuda. Iyeyu anali Mfarisi wotchedwa Gamaliyeli,+ mphunzitsi wa Chilamulo wolemekezedwa ndi anthu onse. Ndiyeno analamula kuti anthuwo awatulutse kwa kanthawi.+