Machitidwe 5:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Koma Mfarisi wina dzina lake Gamaliyeli+ anaimirira mʼKhoti Lalikulu la Ayuda. Iyeyu anali mphunzitsi wa Chilamulo wolemekezedwa ndi anthu onse. Ndiyeno analamula kuti anthuwo awatulutse kwakanthawi. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:34 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 40 Nsanja ya Olonda,5/15/2008, tsa. 319/15/2006, tsa. 9
34 Koma Mfarisi wina dzina lake Gamaliyeli+ anaimirira mʼKhoti Lalikulu la Ayuda. Iyeyu anali mphunzitsi wa Chilamulo wolemekezedwa ndi anthu onse. Ndiyeno analamula kuti anthuwo awatulutse kwakanthawi.