Machitidwe 5:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Koma mwamuna wina anaimirira pa Khoti Lalikulu la Ayuda. Iyeyu anali Mfarisi wotchedwa Gamaliyeli,+ mphunzitsi wa Chilamulo wolemekezedwa ndi anthu onse. Ndiyeno analamula kuti anthuwo awatulutse kwa kanthawi.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:34 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 40 Nsanja ya Olonda,5/15/2008, tsa. 319/15/2006, tsa. 9
34 Koma mwamuna wina anaimirira pa Khoti Lalikulu la Ayuda. Iyeyu anali Mfarisi wotchedwa Gamaliyeli,+ mphunzitsi wa Chilamulo wolemekezedwa ndi anthu onse. Ndiyeno analamula kuti anthuwo awatulutse kwa kanthawi.+