Machitidwe 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Amuna amene anali naye limodzi pa ulendowo,+ anangoima chilili kusowa chonena.+ Iwo anamva ndithu mawuwo,+ koma sanaone munthu aliyense.
7 Amuna amene anali naye limodzi pa ulendowo,+ anangoima chilili kusowa chonena.+ Iwo anamva ndithu mawuwo,+ koma sanaone munthu aliyense.