Machitidwe 22:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Amuna amene anali nane+ anaonadi kuwalako, koma sanamve mawu a amene anali kulankhula ndi ine.+