Machitidwe 24:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma zaka ziwiri zitatha, Felike anachoka ndipo Porikiyo Fesito ndi amene analowa m’malo mwake. Koma popeza kuti Felike ankafuna kuti Ayuda azimukonda,+ anangomusiya m’ndende Paulo.
27 Koma zaka ziwiri zitatha, Felike anachoka ndipo Porikiyo Fesito ndi amene analowa m’malo mwake. Koma popeza kuti Felike ankafuna kuti Ayuda azimukonda,+ anangomusiya m’ndende Paulo.