Machitidwe 24:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndipo ine ndili ndi chiyembekezo+ mwa Mulungu, chimenenso anthu awa ali nacho, kuti kudzakhala kuuka+ kwa olungama+ ndi osalungama omwe.+
15 Ndipo ine ndili ndi chiyembekezo+ mwa Mulungu, chimenenso anthu awa ali nacho, kuti kudzakhala kuuka+ kwa olungama+ ndi osalungama omwe.+