Mateyu 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Atafika kumeneko anakakhala mumzinda wotchedwa Nazareti+ kuti akwaniritsidwe mawu onenedwa kudzera mwa aneneri kuti: “Iye adzatchedwa Mnazareti.”+ Machitidwe 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 dziwani nonsenu ndi Aisiraeli onse, kuti m’dzina la Yesu Khristu Mnazareti+ uja, amene inu munamupachika pamtengo,+ koma amene Mulungu anamuukitsa kwa akufa,+ kudzera mwa iyeyo, munthu uyu waimirira pamaso panu atachira bwinobwino.
23 Atafika kumeneko anakakhala mumzinda wotchedwa Nazareti+ kuti akwaniritsidwe mawu onenedwa kudzera mwa aneneri kuti: “Iye adzatchedwa Mnazareti.”+
10 dziwani nonsenu ndi Aisiraeli onse, kuti m’dzina la Yesu Khristu Mnazareti+ uja, amene inu munamupachika pamtengo,+ koma amene Mulungu anamuukitsa kwa akufa,+ kudzera mwa iyeyo, munthu uyu waimirira pamaso panu atachira bwinobwino.