Machitidwe 14:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pamene khamu la anthu linaona zimene Paulo anachitazo, linafuula ndi kunena m’chinenero cha Chilukaoniya kuti: “Milungu+ yakhala ngati anthu, ndipo yatsikira kwa ife!”
11 Pamene khamu la anthu linaona zimene Paulo anachitazo, linafuula ndi kunena m’chinenero cha Chilukaoniya kuti: “Milungu+ yakhala ngati anthu, ndipo yatsikira kwa ife!”