Aefeso 6:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 umene ndili kazembe+ wake womangidwa ndi unyolo, ndiponso kuti ndilankhule za uthengawo molimba mtima monga mmene ndiyenera kuchitira.+ 2 Timoteyo 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ambuye achitire chifundo banja la Onesiforo,+ chifukwa iye anali kubwera kawirikawiri kudzandilimbikitsa,+ ndipo sanachite manyazi ndi maunyolo anga.+
20 umene ndili kazembe+ wake womangidwa ndi unyolo, ndiponso kuti ndilankhule za uthengawo molimba mtima monga mmene ndiyenera kuchitira.+
16 Ambuye achitire chifundo banja la Onesiforo,+ chifukwa iye anali kubwera kawirikawiri kudzandilimbikitsa,+ ndipo sanachite manyazi ndi maunyolo anga.+