-
Machitidwe 17:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Koma ena anzeru za dziko, Aepikureya ndi Asitoiki+ anayamba kutsutsana naye. Ndipo ena anali kunena kuti: “Kodi nayenso wobwetuka uyu akufuna kunena chiyani?”+ Enanso anali kunena kuti: “Akuoneka kuti ndi wofalitsa za milungu yachilendo.” Ananena zimenezi chifukwa chakuti Paulo anali kulengeza uthenga wabwino wa Yesu ndi za kuuka kwa akufa.+
-