Yohane 18:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho Yudasi anatenga gulu la asilikali ndi alonda ochokera kwa ansembe aakulu ndi kwa Afarisi. Iwo anafika kumeneko atanyamula miyuni, nyale ndi zida.+
3 Choncho Yudasi anatenga gulu la asilikali ndi alonda ochokera kwa ansembe aakulu ndi kwa Afarisi. Iwo anafika kumeneko atanyamula miyuni, nyale ndi zida.+