Genesis 21:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Isaki atakwanitsa masiku 8, Abulahamu anamudula mwana wakeyo, monga mmene Mulungu anamulamulira.+ Levitiko 12:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndipo pa tsiku la 8, khungu la mwanayo lizidulidwa.+ Luka 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Tsopano masiku 8+ atakwanira kuti achite mdulidwe+ wa mwanayo, anamupatsanso dzina lakuti Yesu.+ Dzina limeneli ndi limene mngelo uja anatchula m’mbuyomo, Mariya asanakhale ndi pakati.+
21 Tsopano masiku 8+ atakwanira kuti achite mdulidwe+ wa mwanayo, anamupatsanso dzina lakuti Yesu.+ Dzina limeneli ndi limene mngelo uja anatchula m’mbuyomo, Mariya asanakhale ndi pakati.+