Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 17:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Mwana aliyense wamwamuna amene wakwanitsa masiku 8 azidulidwa+ m’mibadwo yanu yonse. Aliyense wobadwira m’nyumba yanu ndi aliyense wosakhala mbewu yanu koma wogulidwa ndi ndalama kwa mlendo azidulidwa.

  • Genesis 21:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Isaki atakwanitsa masiku 8, Abulahamu anamudula mwana wakeyo, monga mmene Mulungu anamulamulira.+

  • Luka 1:59
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 59 Pa tsiku la 8, iwo anabwera kudzachita mdulidwe wa mwanayo,+ komanso anafuna kum’patsa dzina la bambo ake, lakuti Zekariya.

  • Luka 2:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Tsopano masiku 8+ atakwanira kuti achite mdulidwe+ wa mwanayo, anamupatsanso dzina lakuti Yesu.+ Dzina limeneli ndi limene mngelo uja anatchula m’mbuyomo, Mariya asanakhale ndi pakati.+

  • Yohane 7:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Pa chifukwa chimenechi Mose anakupatsani mdulidwe.+ Sikuti mdulidwewo ndi wochokera kwa Mose ayi, koma ndi wochokera kwa makolo akale,+ ndipo mumachita mdulidwe tsiku la sabata.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena