Genesis 17:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mwana aliyense wamwamuna amene wakwanitsa masiku 8 azidulidwa+ m’mibadwo yanu yonse. Aliyense wobadwira m’nyumba yanu ndi aliyense wosakhala mbewu yanu koma wogulidwa ndi ndalama kwa mlendo azidulidwa. Levitiko 12:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndipo pa tsiku la 8, khungu la mwanayo lizidulidwa.+ Afilipi 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ineyo ndinadulidwa pa tsiku la 8,+ ndine wa mtundu wa Isiraeli, wa fuko la Benjamini,+ Mheberi wobadwa kwa Aheberi.+ Kunena za chilamulo, ndine Mfarisi.+
12 Mwana aliyense wamwamuna amene wakwanitsa masiku 8 azidulidwa+ m’mibadwo yanu yonse. Aliyense wobadwira m’nyumba yanu ndi aliyense wosakhala mbewu yanu koma wogulidwa ndi ndalama kwa mlendo azidulidwa.
5 Ineyo ndinadulidwa pa tsiku la 8,+ ndine wa mtundu wa Isiraeli, wa fuko la Benjamini,+ Mheberi wobadwa kwa Aheberi.+ Kunena za chilamulo, ndine Mfarisi.+