Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 3:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Uike Yoswa kukhala mtsogoleri+ ndipo umulimbikitse ndi kumulimbitsa, chifukwa ndiye adzawolotsa+ anthuwa ndi kuwachititsa kulandira dziko limene ulionelo kukhala cholowa chawo.’+

  • Deuteronomo 31:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Yehova Mulungu wanu akuwoloka patsogolo panu kuti akutsogolereni.+ Iye ndiye adzawononga mitundu imeneyi pamaso panu, ndipo inu mudzaipitikitse.+ Yoswa ndiye adzakutsogolerani ndi kukuwolotsani,+ monga mmene Yehova wanenera.

  • Yoswa 3:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ndipo zimenezi zinachitikadi. Anthuwo anachotsa mahema awo, n’kunyamuka. Anayandikira Yorodano kuti awoloke, ndipo ansembe onyamula likasa+ la pangano anali patsogolo pawo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena