Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 27:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Chotero Yehova anauza Mose kuti: “Tenga Yoswa mwana wa Nuni, munthu wolimba mtima,*+ ndipo uike manja ako pa iye.+

  • Deuteronomo 3:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Uike Yoswa kukhala mtsogoleri+ ndipo umulimbikitse ndi kumulimbitsa, chifukwa ndiye adzawolotsa+ anthuwa ndi kuwachititsa kulandira dziko limene ulionelo kukhala cholowa chawo.’+

  • Yoswa 1:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Mose mtumiki wanga wamwalira.+ Tsopano konzeka limodzi ndi anthu onsewa, kuti muwoloke Yorodanoyu ndi kulowa m’dziko limene ndikulipereka kwa ana a Isiraeli.+

  • Yoswa 4:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Pa tsikuli, Yehova anachititsa Yoswa kukhala wamkulu m’maso mwa Aisiraeli onse,+ ndipo anayamba kumuopa monga mmene anaopera Mose masiku onse a moyo wake.+

  • Machitidwe 7:45
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 45 Ndipo makolo athu amene anachilandira kwa makolo awo, analowa nacho limodzi ndi Yoswa,+ m’dziko limene linali m’manja mwa anthu a mitundu ina+ amene Mulungu anawapitikitsa pamaso pa makolo athu.+ Chihemacho chinakhala m’dziko limeneli mpaka m’masiku a Davide.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena