Yoswa 23:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova adzapitikitsa mitundu ikuluikulu ndiponso yamphamvu kuichotsa pamaso panu.+ (Kufikira lero, palibe munthu ngakhale mmodzi amene wakwanitsa kulimbana nanu.)+ Yoswa 24:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Yehova anathamangitsa mitundu yonse ya anthu+ pamaso pathu, ngakhale Aamori amene anali kukhala m’dzikoli. Choncho, nafenso tizitumikira Yehova chifukwa iye ndi Mulungu wathu.”+
9 Yehova adzapitikitsa mitundu ikuluikulu ndiponso yamphamvu kuichotsa pamaso panu.+ (Kufikira lero, palibe munthu ngakhale mmodzi amene wakwanitsa kulimbana nanu.)+
18 Yehova anathamangitsa mitundu yonse ya anthu+ pamaso pathu, ngakhale Aamori amene anali kukhala m’dzikoli. Choncho, nafenso tizitumikira Yehova chifukwa iye ndi Mulungu wathu.”+