Deuteronomo 34:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yoswa mwana wa Nuni anali wodzazidwa ndi mzimu wa nzeru,+ pakuti Mose anaika manja ake pa iye.+ Choncho ana a Isiraeli anayamba kumumvera ndipo iwo anayamba kuchita monga momwe Yehova analamulira Mose.+ Machitidwe 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno anawaimiritsa pamaso pa atumwiwo, ndipo atapemphera, atumwiwo anaika manja+ awo pa iwo. 1 Timoteyo 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Usamanyalanyaze mphatso+ imene uli nayo, yomwe unapatsidwa mwaulosi+ ndiponso pamene bungwe la akulu linaika manja+ pa iwe.
9 Yoswa mwana wa Nuni anali wodzazidwa ndi mzimu wa nzeru,+ pakuti Mose anaika manja ake pa iye.+ Choncho ana a Isiraeli anayamba kumumvera ndipo iwo anayamba kuchita monga momwe Yehova analamulira Mose.+
14 Usamanyalanyaze mphatso+ imene uli nayo, yomwe unapatsidwa mwaulosi+ ndiponso pamene bungwe la akulu linaika manja+ pa iwe.