Yohane 15:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 ndipo inunso mudzachitira umboni,+ chifukwa mwakhala nane kuchokera pa chiyambi.