Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Luka 1:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Iwo analemba ndendende mmene anatiuzira anthu amene anakhala mboni zoona ndi maso+ ndi atumiki a uthengawo+ kuchokera pa chiyambi.+

  • Luka 24:48
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 48 inu mudzakhala mboni+ za zimenezi.

  • Machitidwe 1:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Koma mzimu woyera ukadzafika pa inu, mudzalandira mphamvu.+ Pamenepo mudzakhala mboni+ zanga mu Yerusalemu,+ ku Yudeya konse ndi ku Samariya,+ mpaka kumalekezero a dziko lapansi.”+

  • Machitidwe 2:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 “Amuna inu a mu Isiraeli, imvani mawu awa: Yesu Mnazareti,+ ndi munthu amene Mulungu anamuonetsera poyera kwa inu. Anatero mwa ntchito zamphamvu,+ mwa zodabwitsa komanso mwa zizindikiro, zimene Mulungu anachita pakati panu kudzera mwa iye,+ monga mmene inunso mukudziwira.

  • Machitidwe 5:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Ndipo ife ndife mboni za zinthu zimenezi,+ chimodzimodzinso mzimu woyera,+ umene Mulungu wapereka kwa anthu omumvera monga wolamulira.”

  • 1 Petulo 5:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Choncho, ndikulangiza akulu amene ali pakati panu mowadandaulira, pakuti inenso ndine mkulu+ ngati iwowo. Ndinenso mboni+ ya masautso a Khristu, ndiponso ndidzalandira nawo ulemerero umene udzaonekere.+ Kwa iwo ndikuti:

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena