1 Petulo 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Choncho, ine monga mkulu mnzanu, amene ndinaona mmene Khristu anavutikira komanso ndikuyembekezera kudzalandira nawo ulemerero umene udzaonekere,+ ndikupempha akulu amene ali pakati panu kuti: 1 Petulo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:1 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 20 Nsanja ya Olonda,6/15/2011, tsa. 20
5 Choncho, ine monga mkulu mnzanu, amene ndinaona mmene Khristu anavutikira komanso ndikuyembekezera kudzalandira nawo ulemerero umene udzaonekere,+ ndikupempha akulu amene ali pakati panu kuti: