1 Petulo 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Choncho, ndikulangiza akulu amene ali pakati panu mowadandaulira, pakuti inenso ndine mkulu+ ngati iwowo. Ndinenso mboni+ ya masautso a Khristu, ndiponso ndidzalandira nawo ulemerero umene udzaonekere.+ Kwa iwo ndikuti: 1 Petulo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:1 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 20 Nsanja ya Olonda,6/15/2011, tsa. 20
5 Choncho, ndikulangiza akulu amene ali pakati panu mowadandaulira, pakuti inenso ndine mkulu+ ngati iwowo. Ndinenso mboni+ ya masautso a Khristu, ndiponso ndidzalandira nawo ulemerero umene udzaonekere.+ Kwa iwo ndikuti: