2 Yohane 1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Ine monga mkulu,+ ndikulembera mayi wosankhidwa+ ndi Mulungu ndiponso ana ake amene ndimawakondadi.+ Ndipo si ine ndekha amene ndimawakonda. Onse amene adziwa choonadi amawakondanso.+
1 Ine monga mkulu,+ ndikulembera mayi wosankhidwa+ ndi Mulungu ndiponso ana ake amene ndimawakondadi.+ Ndipo si ine ndekha amene ndimawakonda. Onse amene adziwa choonadi amawakondanso.+