Aroma 8:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiye chifukwa chake ndikuona kuti masautso+ amene tili nawo tsopano si kanthu powayerekeza ndi ulemerero+ umene udzaonekere kudzera mwa ife.
18 Ndiye chifukwa chake ndikuona kuti masautso+ amene tili nawo tsopano si kanthu powayerekeza ndi ulemerero+ umene udzaonekere kudzera mwa ife.