Luka 24:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 inu mudzakhala mboni+ za zimenezi. Machitidwe 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma mzimu woyera ukadzafika pa inu, mudzalandira mphamvu.+ Pamenepo mudzakhala mboni+ zanga mu Yerusalemu,+ ku Yudeya konse ndi ku Samariya,+ mpaka kumalekezero a dziko lapansi.”+ Machitidwe 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Wotenga malo amenewa akhale munthu amene wakhala akusonkhana nafe kuyambira pamene Yesu anabatizidwa+ ndi Yohane, kudzafika tsiku limene anatengedwa kupita kumwamba kuchoka pakati pathu.+ Mmodzi wa amuna amenewa, akhale mboni ya kuuka kwake pamodzi ndi ife.”+
8 Koma mzimu woyera ukadzafika pa inu, mudzalandira mphamvu.+ Pamenepo mudzakhala mboni+ zanga mu Yerusalemu,+ ku Yudeya konse ndi ku Samariya,+ mpaka kumalekezero a dziko lapansi.”+
22 Wotenga malo amenewa akhale munthu amene wakhala akusonkhana nafe kuyambira pamene Yesu anabatizidwa+ ndi Yohane, kudzafika tsiku limene anatengedwa kupita kumwamba kuchoka pakati pathu.+ Mmodzi wa amuna amenewa, akhale mboni ya kuuka kwake pamodzi ndi ife.”+