Mateyu 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kenako Yesu anabwera kwa Yohane ku Yorodano kuchokera ku Galileya,+ kuti iye amubatize.+ Machitidwe 10:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Inu mukudziwa nkhani imene inali m’kamwam’kamwa mu Yudeya monse, kuyambira ku Galileya pambuyo pa ubatizo umene Yohane anali kulalikira.+
37 Inu mukudziwa nkhani imene inali m’kamwam’kamwa mu Yudeya monse, kuyambira ku Galileya pambuyo pa ubatizo umene Yohane anali kulalikira.+