Machitidwe 10:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Inu mukudziwa nkhani imene inali mʼkamwamʼkamwa kuyambira ku Galileya+ mpaka ku Yudeya konse, pambuyo pa ubatizo umene Yohane ankalalikira.
37 Inu mukudziwa nkhani imene inali mʼkamwamʼkamwa kuyambira ku Galileya+ mpaka ku Yudeya konse, pambuyo pa ubatizo umene Yohane ankalalikira.