Machitidwe 10:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Inu mukudziwa nkhani imene inali m’kamwam’kamwa mu Yudeya monse, kuyambira ku Galileya pambuyo pa ubatizo umene Yohane anali kulalikira.+
37 Inu mukudziwa nkhani imene inali m’kamwam’kamwa mu Yudeya monse, kuyambira ku Galileya pambuyo pa ubatizo umene Yohane anali kulalikira.+