Machitidwe 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Munthu wake akhale amene ankayenda nafe kuyambira pamene Yesu anabatizidwa ndi Yohane,+ kudzafika tsiku limene anatengedwa kupita kumwamba kuchoka pakati pathu.+ Munthu ameneyu akhale mboni ya kuuka kwa Yesu pamodzi ndi ife.”+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:22 Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 18-19
22 Munthu wake akhale amene ankayenda nafe kuyambira pamene Yesu anabatizidwa ndi Yohane,+ kudzafika tsiku limene anatengedwa kupita kumwamba kuchoka pakati pathu.+ Munthu ameneyu akhale mboni ya kuuka kwa Yesu pamodzi ndi ife.”+