Machitidwe 13:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iwo anayenda pachilumba chonsecho mpaka kukafika ku Pafo. Kumeneko anakumana ndi munthu wina wamatsenga. Munthu ameneyu anali Myuda dzina lake Bara-Yesu, ndipo analinso mneneri wonyenga.+
6 Iwo anayenda pachilumba chonsecho mpaka kukafika ku Pafo. Kumeneko anakumana ndi munthu wina wamatsenga. Munthu ameneyu anali Myuda dzina lake Bara-Yesu, ndipo analinso mneneri wonyenga.+