Mateyu 13:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Kenako anawauza kuti: “Popeza kuti zili choncho, mphunzitsi aliyense wa anthu akaphunzitsidwa za ufumu wakumwamba,+ amakhala ngati munthu, mwininyumba, amene amatulutsa zinthu zatsopano ndi zakale mosungiramo chuma chake.”+
52 Kenako anawauza kuti: “Popeza kuti zili choncho, mphunzitsi aliyense wa anthu akaphunzitsidwa za ufumu wakumwamba,+ amakhala ngati munthu, mwininyumba, amene amatulutsa zinthu zatsopano ndi zakale mosungiramo chuma chake.”+