Mateyu 12:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Munthu wabwino amatulutsa zabwino m’chuma chake chabwino,+ koma munthu woipa amatulutsa zoipa m’chuma chake choipa.+ Luka 6:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Munthu wabwino amatulutsa zabwino m’chuma chabwino+ cha mtima wake. Koma munthu woipa amatulutsa zoipa m’chuma chake choipa, pakuti pakamwa pamalankhula zosefukira mumtima.+
35 Munthu wabwino amatulutsa zabwino m’chuma chake chabwino,+ koma munthu woipa amatulutsa zoipa m’chuma chake choipa.+
45 Munthu wabwino amatulutsa zabwino m’chuma chabwino+ cha mtima wake. Koma munthu woipa amatulutsa zoipa m’chuma chake choipa, pakuti pakamwa pamalankhula zosefukira mumtima.+