Machitidwe 21:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 M’mawa mwake tinanyamuka ndi kukafika ku Kaisareya.+ Kumeneko tinakalowa m’nyumba ya mlaliki* Filipo. Iyeyu anali mmodzi wa amuna 7 a mbiri yabwino aja,+ ndipo tinakhala naye.
8 M’mawa mwake tinanyamuka ndi kukafika ku Kaisareya.+ Kumeneko tinakalowa m’nyumba ya mlaliki* Filipo. Iyeyu anali mmodzi wa amuna 7 a mbiri yabwino aja,+ ndipo tinakhala naye.