Levitiko 23:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kuchokera pa tsiku limene sabata la 7 lakwanira, pazidutsa masiku 50,+ ndipo muzipereka nsembe yambewu zatsopano+ kwa Yehova. Deuteronomo 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Uziwerenga masabata 7. Uziyamba kuwerenga masabata 7 amenewo kuchokera pamene wayamba kumweta tirigu.+
16 Kuchokera pa tsiku limene sabata la 7 lakwanira, pazidutsa masiku 50,+ ndipo muzipereka nsembe yambewu zatsopano+ kwa Yehova.
9 “Uziwerenga masabata 7. Uziyamba kuwerenga masabata 7 amenewo kuchokera pamene wayamba kumweta tirigu.+