Machitidwe 13:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Ndipo ophunzirawo anapitiriza kudzazidwa ndi chimwemwe+ ndi mzimu woyera. Machitidwe 22:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 anabwera kwa ine. Ataima pafupi nane, anati, ‘M’bale wanga Saulo, yambanso kuona!’+ Nthawi yomweyo ndinakweza maso anga kumuyang’ana.
13 anabwera kwa ine. Ataima pafupi nane, anati, ‘M’bale wanga Saulo, yambanso kuona!’+ Nthawi yomweyo ndinakweza maso anga kumuyang’ana.