Mateyu 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kondwerani, dumphani ndi chimwemwe,+ chifukwa mphoto+ yanu ndi yaikulu kumwamba, pakuti umu ndi mmenenso anazunzira aneneri+ amene analipo inu musanakhaleko. 1 Atesalonika 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho munatsanzira+ ifeyo komanso munatsanzira Ambuye,+ pakuti munalandira mawuwo ndi chimwemwe cha mzimu woyera+ ngakhale kuti munali m’masautso+ ambiri,
12 Kondwerani, dumphani ndi chimwemwe,+ chifukwa mphoto+ yanu ndi yaikulu kumwamba, pakuti umu ndi mmenenso anazunzira aneneri+ amene analipo inu musanakhaleko.
6 Choncho munatsanzira+ ifeyo komanso munatsanzira Ambuye,+ pakuti munalandira mawuwo ndi chimwemwe cha mzimu woyera+ ngakhale kuti munali m’masautso+ ambiri,