1 Timoteyo 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma azidzikongoletsa mogwirizana ndi mmene akazi amene amati amalemekeza Mulungu amayenera kudzikongoletsera.+ Azidzikongoletsa ndi ntchito zabwino.+
10 Koma azidzikongoletsa mogwirizana ndi mmene akazi amene amati amalemekeza Mulungu amayenera kudzikongoletsera.+ Azidzikongoletsa ndi ntchito zabwino.+